Yesaya 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Dzikolo likudzandira ngati munthu woledzera.Likugwedezekera uku ndi uku ngati chisimba* chimene chikugwedezeka ndi mphepo. Dzikolo lalemedwa ndi zolakwa zake,+Ndipo lidzagwa moti silidzadzukanso. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:20 Yesaya 1, ptsa. 266, 267-268
20 Dzikolo likudzandira ngati munthu woledzera.Likugwedezekera uku ndi uku ngati chisimba* chimene chikugwedezeka ndi mphepo. Dzikolo lalemedwa ndi zolakwa zake,+Ndipo lidzagwa moti silidzadzukanso.