-
Yesaya 24:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Iwo adzasonkhanitsidwa pamodzi
Ngati akaidi amene akuwasonkhanitsira mʼdzenje,
Ndipo adzatsekeredwa mʼndende,
Pambuyo pa masiku ochuluka adzakumbukiridwanso.
-