-
Yesaya 26:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka, mzinda wokwezeka.
Mzindawo wautsitsa,
Wautsitsira pansi,
Waugwetsera pafumbi.
-