Yesaya 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, pamene tikutsatira njira ya ziweruzo zanu,Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tikulakalaka dzina lanu komanso zimene dzinalo limaimira.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:8 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 19 Yesaya 1, tsa. 279
8 Inu Yehova, pamene tikutsatira njira ya ziweruzo zanu,Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tikulakalaka dzina lanu komanso zimene dzinalo limaimira.*