Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezedwa, koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona kuti mumakonda kwambiri anthu anu* ndipo adzachita manyazi. Inde, moto wanu udzapsereza adani anu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:11 Yesaya 1, tsa. 280
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezedwa, koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona kuti mumakonda kwambiri anthu anu* ndipo adzachita manyazi. Inde, moto wanu udzapsereza adani anu.