Yesaya 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine Yehova ndikulondera mkaziyo.+ Ndimamuthirira nthawi zonse.+ Ndimamulondera masana ndi usiku,Kuti wina aliyense asamuvulaze.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:3 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, ptsa. 21-22 Yesaya 1, ptsa. 284-286
3 Ine Yehova ndikulondera mkaziyo.+ Ndimamuthirira nthawi zonse.+ Ndimamulondera masana ndi usiku,Kuti wina aliyense asamuvulaze.+