Yesaya 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku limenelo nyanga yaikulu ya nkhosa idzalizidwa,+ ndipo anthu amene anali atatsala pangʼono kufa mʼdziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana mʼdziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira Yehova mʼphiri loyera ku Yerusalemu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:13 Yesaya 1, tsa. 285
13 Pa tsiku limenelo nyanga yaikulu ya nkhosa idzalizidwa,+ ndipo anthu amene anali atatsala pangʼono kufa mʼdziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana mʼdziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira Yehova mʼphiri loyera ku Yerusalemu.+