Yesaya 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsoka kwa chisoti* chokongola* cha zidakwa za ku Efuraimu+Komanso maluwa ake okongola amene akufota!Maluwawo avalidwa ndi mzinda umene uli paphiri, pamwamba pa chigwa chachonde, kumene zidakwa zoledzera ndi vinyozo zimakhala. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:1 Yesaya 1, ptsa. 287-288 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, tsa. 11
28 Tsoka kwa chisoti* chokongola* cha zidakwa za ku Efuraimu+Komanso maluwa ake okongola amene akufota!Maluwawo avalidwa ndi mzinda umene uli paphiri, pamwamba pa chigwa chachonde, kumene zidakwa zoledzera ndi vinyozo zimakhala.