Yesaya 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi iliyonse imene akudutsa,Azidzakukokololani.+Chifukwa azidzadutsa mʼmawa uliwonse,Azidzadutsanso masana komanso usiku. Zinthu zochititsa mantha ndi zimene zidzawathandize kumvetsa zimene anamva.”* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:19 Yesaya 1, tsa. 294 Nsanja ya Olonda,6/1/1991, ptsa. 19-20
19 Nthawi iliyonse imene akudutsa,Azidzakukokololani.+Chifukwa azidzadutsa mʼmawa uliwonse,Azidzadutsanso masana komanso usiku. Zinthu zochititsa mantha ndi zimene zidzawathandize kumvetsa zimene anamva.”*