Yesaya 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kodi wolima munda ndi pulawo amangokhalira kulima tsiku lonse osadzala mbewu? Kodi amangokhalira kuphwanya zibuma ndi kusalaza dothi?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:24 Nsanja ya Olonda,10/1/2001, tsa. 11
24 Kodi wolima munda ndi pulawo amangokhalira kulima tsiku lonse osadzala mbewu? Kodi amangokhalira kuphwanya zibuma ndi kusalaza dothi?+