Yesaya 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsoka kwa Ariyeli!* Tsoka kwa Ariyeli, mzinda umene Davide anamangako msasa.+ Pitirizani kuchita zikondwerero+ zanu nthawi zonseMuzichita zimenezi chaka ndi chaka. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:1 Yesaya 1, ptsa. 296-297
29 “Tsoka kwa Ariyeli!* Tsoka kwa Ariyeli, mzinda umene Davide anamangako msasa.+ Pitirizani kuchita zikondwerero+ zanu nthawi zonseMuzichita zimenezi chaka ndi chaka.