-
Yesaya 29:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Inde, zidzachitika ngati mmene zimakhalira munthu wanjala akamalota kuti akudya,
Koma nʼkudzuka ali ndi njala.
Kapena ngati mmene zimakhalira munthu waludzu akamalota kuti akumwa madzi,
Koma nʼkudzuka atatopa komanso ali ndi ludzu.
Zidzakhalanso choncho ndi gulu la mitundu yonse
Imene ikuchita nkhondo ndi phiri la Ziyoni.+
-