-
Yesaya 29:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndipo bukulo akalipereka kwa munthu wosadziwa kuwerenga nʼkumuuza kuti: “Werenga bukuli,” iye adzayankha kuti: “Sindidziwa kuwerenga ngakhale pangʼono.”
-