Yesaya 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wanena kuti: “Anthu awa amandiyandikira ndi pakamwa pawo pokhaNdipo amandilemekeza ndi milomo yawo yokha,+Koma mitima yawo aiika kutali ndi ine,Ndiponso amandiopa chifukwa cha malamulo a anthu amene anaphunzitsidwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:13 Yesaya 1, ptsa. 299, 301
13 Yehova wanena kuti: “Anthu awa amandiyandikira ndi pakamwa pawo pokhaNdipo amandilemekeza ndi milomo yawo yokha,+Koma mitima yawo aiika kutali ndi ine,Ndiponso amandiopa chifukwa cha malamulo a anthu amene anaphunzitsidwa.+