Yesaya 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsiku limenelo, anthu amene ali ndi vuto losamva adzamva mawu amʼbuku,Ndipo maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzamasuka kumdima wandiweyani ndipo adzayamba kuona.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:18 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, ptsa. 232-233, 235 Yesaya 1, ptsa. 298, 300
18 Tsiku limenelo, anthu amene ali ndi vuto losamva adzamva mawu amʼbuku,Ndipo maso a anthu amene ali ndi vuto losaona adzamasuka kumdima wandiweyani ndipo adzayamba kuona.+