Yesaya 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Thanthwe lake lidzachoka chifukwa cha mantha,Ndipo akalonga ake adzachita mantha chifukwa cha chizindikiro,” akutero Yehova,Amene kuwala kwake kuli mu Ziyoni* ndiponso amene ngʼanjo yake ili mu Yerusalemu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:9 Yesaya 1, tsa. 328
9 Thanthwe lake lidzachoka chifukwa cha mantha,Ndipo akalonga ake adzachita mantha chifukwa cha chizindikiro,” akutero Yehova,Amene kuwala kwake kuli mu Ziyoni* ndiponso amene ngʼanjo yake ili mu Yerusalemu.