Yesaya 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wa anthu opupuluma udzaganizira mofatsa kuti udziwe zinthu,Ndipo ngakhale lilime la anthu achibwibwi lidzalankhula bwinobwino komanso zinthu zomveka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:4 Yesaya 1, tsa. 335
4 Mtima wa anthu opupuluma udzaganizira mofatsa kuti udziwe zinthu,Ndipo ngakhale lilime la anthu achibwibwi lidzalankhula bwinobwino komanso zinthu zomveka.+