Yesaya 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Inu akazi ochita zinthu motayirira, nyamukani ndipo mvetserani mawu anga! Inu ana aakazi osasamala,+ mvetserani zimene ndikunena! Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:9 Yesaya 1, ptsa. 338-339
9 “Inu akazi ochita zinthu motayirira, nyamukani ndipo mvetserani mawu anga! Inu ana aakazi osasamala,+ mvetserani zimene ndikunena!