Yesaya 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakangodutsa chaka chimodzi, inu amene mumachita zinthu mosasamala mudzadzidzimuka,Chifukwa sipadzakhala mphesa zilizonse zimene zasonkhanitsidwa ngakhale nyengo yokolola mphesa itatha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:10 Yesaya 1, ptsa. 338-339
10 Pakangodutsa chaka chimodzi, inu amene mumachita zinthu mosasamala mudzadzidzimuka,Chifukwa sipadzakhala mphesa zilizonse zimene zasonkhanitsidwa ngakhale nyengo yokolola mphesa itatha.+