-
Yesaya 34:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Kumeneko, njoka yodumpha idzakonzako chisa chake nʼkuikira mazira,
Ndipo idzaswa tiana nʼkutisonkhanitsa pansi pa mthunzi wake.
Inde, mbalame zotchedwa akamtema zidzasonkhana kumeneko, iliyonse ndi mwamuna wake.
-