-
Yesaya 34:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Fufuzani mʼbuku la Yehova ndipo muwerenge mokweza:
Palibe ndi imodzi yomwe imene idzasowe.
Palibe imene idzasowe mwamuna,
Chifukwa pakamwa pa Yehova ndi pamene palamula,
Ndipo mzimu wake ndi umene wazisonkhanitsa pamodzi.
-