-
Yesaya 36:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Musamvere Hezekiya chifukwa mfumu ya Asuri yanena kuti: “Tiyeni tigwirizane zamtendere ndipo ingonenani kuti mwagonja. Mukatero, aliyense azidya zochokera mumtengo wake wa mpesa ndi mumtengo wake wa mkuyu komanso azimwa madzi apachitsime chake,
-