Yesaya 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiika maganizo* mwa iye ndipo adzamva nkhani inayake nʼkubwerera kudziko lake.+ Ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga mʼdziko lakelo.”’”+
7 Ndiika maganizo* mwa iye ndipo adzamva nkhani inayake nʼkubwerera kudziko lake.+ Ndidzachititsa kuti akaphedwe ndi lupanga mʼdziko lakelo.”’”+