Yesaya 37:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nʼzoonadi Yehova, kuti mafumu a Asuri awononga mayiko onse,+ ndi dziko lawo lomwe.