-
Yesaya 37:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Anthu okhala mʼmizindayo adzafooka.
Adzachita mantha ndiponso adzachititsidwa manyazi.
Adzakhala ngati zomera zakutchire komanso ngati udzu wanthete wobiriwira,
Ngati udzu womera padenga umene wawauka ndi mphepo yotentha yakumʼmawa.
-