Yesaya 38:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Bwerera kwa Hezekiya+ ndipo ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndipo ndaona misozi yako.+ Tsopano ndiwonjezera zaka 15 pa moyo wako,*+
5 “Bwerera kwa Hezekiya+ ndipo ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Davide kholo lako wanena kuti: “Ndamva pemphero lako+ ndipo ndaona misozi yako.+ Tsopano ndiwonjezera zaka 15 pa moyo wako,*+