Yesaya 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Inu Yehova, munthu aliyense amakhala ndi moyo chifukwa cha zinthu zimenezi,*Ndipo mʼzinthu zimenezi, mzimu wanga umapezamo moyo. Inu mudzabwezeretsa thanzi langa nʼkundithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+
16 ‘Inu Yehova, munthu aliyense amakhala ndi moyo chifukwa cha zinthu zimenezi,*Ndipo mʼzinthu zimenezi, mzimu wanga umapezamo moyo. Inu mudzabwezeretsa thanzi langa nʼkundithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+