Yesaya 40:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Udzu wobiriwirawo umaumaNdipo maluwawo amafota,+Chifukwa mpweya* wa Yehova umauzira zinthu zimenezi.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.
7 Udzu wobiriwirawo umaumaNdipo maluwawo amafota,+Chifukwa mpweya* wa Yehova umauzira zinthu zimenezi.+ Ndithu anthu ali ngati udzu wobiriwira.