Yesaya 40:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsa zinthu?Ndi ndani amene amamuphunzitsa njira yachilungamo,Kapena kumuphunzitsa kuti adziwe zinthu,Kapenanso kumusonyeza njira yokhalira womvetsadi zinthu?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:14 Yesaya 1, ptsa. 407-408
14 Kodi anafunsirapo nzeru kwa ndani kuti amuthandize kumvetsa zinthu?Ndi ndani amene amamuphunzitsa njira yachilungamo,Kapena kumuphunzitsa kuti adziwe zinthu,Kapenanso kumusonyeza njira yokhalira womvetsadi zinthu?+