Yesaya 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko,Ndipo iye amawaona ngati fumbi limene lili pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba ngati akunyamula fumbi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 40:15 Yesaya 1, ptsa. 408-409
15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko,Ndipo iye amawaona ngati fumbi limene lili pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba ngati akunyamula fumbi.