Yesaya 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kodi simukudziwa? Kodi simunamve? Kodi simunauzidwe kuchokera pachiyambi? Kodi simunamvetse umboni umene wakhalapo kuchokera pamene maziko a dziko lapansi anakhazikitsidwa?+
21 Kodi simukudziwa? Kodi simunamve? Kodi simunauzidwe kuchokera pachiyambi? Kodi simunamvetse umboni umene wakhalapo kuchokera pamene maziko a dziko lapansi anakhazikitsidwa?+