Yesaya 41:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndinali woyamba kuuza Ziyoni kuti: “Tamverani zimene zidzachitike!”+ Ndipo ku Yerusalemu ndidzatumizako munthu wobweretsa uthenga wabwino.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:27 Yesaya 2, tsa. 29
27 Ine ndinali woyamba kuuza Ziyoni kuti: “Tamverani zimene zidzachitike!”+ Ndipo ku Yerusalemu ndidzatumizako munthu wobweretsa uthenga wabwino.+