-
Yesaya 41:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma ndinapitiriza kuyangʼana, ndipo panalibe aliyense.
Pakati pa mafanowo panalibe aliyense amene akanapereka malangizo.
Ndipo ndinapitiriza kuwafunsa, koma palibe anayankha.
-