Yesaya 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye sadzafooka kapena kutaya mtima mpaka atakhazikitsa chilungamo padziko lapansi.+Ndipo zilumba zikudikirirabe malamulo ake.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:4 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 80-81 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 23 Yesaya 2, ptsa. 30-31, 37
4 Iye sadzafooka kapena kutaya mtima mpaka atakhazikitsa chilungamo padziko lapansi.+Ndipo zilumba zikudikirirabe malamulo ake.*