Yesaya 42:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuti ukatsegule maso a anthu amene ali ndi vuto losaona,+Kuti ukatulutse mkaidi mʼdzenje lamdimaNdiponso kuti anthu amene ali mumdima akawatulutse mʼndende.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:7 Nsanja ya Olonda,1/15/2009, tsa. 24 Yesaya 2, ptsa. 37-41
7 Kuti ukatsegule maso a anthu amene ali ndi vuto losaona,+Kuti ukatulutse mkaidi mʼdzenje lamdimaNdiponso kuti anthu amene ali mumdima akawatulutse mʼndende.+