-
Yesaya 42:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mulungu wanena kuti: “Ndakhala chete kwa nthawi yaitali.
Ndinangokhala phee osachita chilichonse.
Mofanana ndi mkazi amene akubereka,
Ndibuula, ndipuma movutikira komanso mwawefuwefu. Zonsezi zichitika nthawi imodzi.
-