Yesaya 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano izi ndi zimene Yehova wanena,Mlengi wako iwe Yakobo, amene anakupanga iwe Isiraeli.+ Iye wanena kuti: “Usachite mantha, chifukwa ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina lako. Iwe ndiwe wanga. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 43:1 Yesaya 2, ptsa. 46-48
43 Tsopano izi ndi zimene Yehova wanena,Mlengi wako iwe Yakobo, amene anakupanga iwe Isiraeli.+ Iye wanena kuti: “Usachite mantha, chifukwa ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina lako. Iwe ndiwe wanga.