Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+Ndiponso amene anakuumba,Amene wakhala akukuthandiza kuyambira uli mʼmimba,* wanena kuti: ‘Usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo,+Ndiponso iwe Yesuruni,*+ amene ndakusankha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:2 Yesaya 2, tsa. 62
2 Yehova, amene anakupanga+Ndiponso amene anakuumba,Amene wakhala akukuthandiza kuyambira uli mʼmimba,* wanena kuti: ‘Usachite mantha, iwe mtumiki wanga Yakobo,+Ndiponso iwe Yesuruni,*+ amene ndakusankha.