-
Yesaya 44:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Hafu ya mtengowo waiwotcha pamoto.
Mtengo umene wauwotcha pamotowo wawotchera nyama imene wadya ndipo wakhuta.
Wawothanso moto wake ndipo wanena kuti:
“Eya! Ndamva kutenthera. Ndaona kuwala kwa moto.”
-