Yesaya 45:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere. Mubwere pamodzi, inu anthu amene mwapulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula zifaniziro zawo zogoba sadziwa chilichonseNdipo amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:20 Yesaya 2, ptsa. 90-91
20 Sonkhanani pamodzi ndipo mubwere. Mubwere pamodzi, inu anthu amene mwapulumuka ku mitundu ya anthu.+ Amene amanyamula zifaniziro zawo zogoba sadziwa chilichonseNdipo amapemphera kwa mulungu woti sangawapulumutse.+