Yesaya 47:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu adzaona maliseche ako. Manyazi ako adzaonekera. Ine ndidzabwezera+ ndipo palibe amene adzanditsekereze.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:3 Yesaya 2, ptsa. 107-108
3 Anthu adzaona maliseche ako. Manyazi ako adzaonekera. Ine ndidzabwezera+ ndipo palibe amene adzanditsekereze.*