Yesaya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:6 Yesaya 2, ptsa. 108-109
6 Ine ndinakwiyira anthu anga.+ Ndinalola kuti cholowa changa chidetsedwe+Ndipo ndinawapereka mʼmanja mwako.+ Koma iwe sunawachitire chifundo.+ Ngakhale munthu wokalamba unamusenzetsa goli lolemera kwambiri.+