Yesaya 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwe unanena kuti: “Nthawi zonse ine ndidzakhala Dona* mpaka kalekale.”+ Sunaganizire zinthu zimenezi mumtima mwako.Sunaganizire kuti zidzatha bwanji. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:7 Yesaya 2, ptsa. 109-110
7 Iwe unanena kuti: “Nthawi zonse ine ndidzakhala Dona* mpaka kalekale.”+ Sunaganizire zinthu zimenezi mumtima mwako.Sunaganizire kuti zidzatha bwanji.