-
Yesaya 47:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iwe unkadalira zoipa zimene unkachita.
Unkanena kuti: “Palibe amene akundiona.”
Nzeru zako komanso kudziwa zinthu ndi zimene zinakusocheretsa,
Ndipo mumtima mwako umanena kuti: “Ndine ndekha, palibenso wina.”
-