Yesaya 47:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Umu ndi mmene amatsenga ako adzakhalireAmene wakhala ukuvutikira nawo limodzi kuyambira uli mwana. Iwo adzabalalika, aliyense kulowera njira yake* Ndipo sipadzakhala aliyense woti akupulumutse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 47:15 Yesaya 2, tsa. 115
15 Umu ndi mmene amatsenga ako adzakhalireAmene wakhala ukuvutikira nawo limodzi kuyambira uli mwana. Iwo adzabalalika, aliyense kulowera njira yake* Ndipo sipadzakhala aliyense woti akupulumutse.+