Yesaya 49:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova amene anandipanga ndili mʼmimba kuti ndikhale mtumiki wake,Wandiuza kuti nditenge Yakobo nʼkumubwezera kwa iye,Nʼcholinga choti Isiraeli asonkhanitsidwe kwa iye.+ Ine ndidzalemekezedwa pamaso pa YehovaNdipo Mulungu wanga adzakhala mphamvu yanga. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:5 Yesaya 2, ptsa. 140-141
5 Ndiyeno Yehova amene anandipanga ndili mʼmimba kuti ndikhale mtumiki wake,Wandiuza kuti nditenge Yakobo nʼkumubwezera kwa iye,Nʼcholinga choti Isiraeli asonkhanitsidwe kwa iye.+ Ine ndidzalemekezedwa pamaso pa YehovaNdipo Mulungu wanga adzakhala mphamvu yanga.