Yesaya 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira. Onse akusonkhana pamodzi.+ Akubwera kwa iwe. Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,Onsewo udzadzikongoletsa nawo ngati zokongoletsera,Ndipo udzawavala ngati ndiwe mkwatibwi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:18 Yesaya 2, ptsa. 147-148
18 Kweza maso ako uone zonse zimene zikuchitika mokuzungulira. Onse akusonkhana pamodzi.+ Akubwera kwa iwe. Yehova wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,Onsewo udzadzikongoletsa nawo ngati zokongoletsera,Ndipo udzawavala ngati ndiwe mkwatibwi.