Yesaya 49:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale kuti malo ako anawonongedwa komanso kusakazidwa ndipo dziko lako linali mabwinja,+Tsopano anthu amene adzakhale mmenemo malo adzawachepera moti adzakhala mopanikizana,+Ndipo anthu amene anakumeza+ adzakhala kutali.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:19 Yesaya 2, ptsa. 147-148
19 Ngakhale kuti malo ako anawonongedwa komanso kusakazidwa ndipo dziko lako linali mabwinja,+Tsopano anthu amene adzakhale mmenemo malo adzawachepera moti adzakhala mopanikizana,+Ndipo anthu amene anakumeza+ adzakhala kutali.+