Yesaya 49:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yehova akunena kuti: “Ngakhale anthu amene agwidwa ndi munthu wamphamvu adzalandidwa,+Ndipo amene anagwidwa ndi wolamulira wankhanza adzapulumutsidwa.+ Ndidzalimbana ndi aliyense amene akulimbana nawe,+Ndipo ana ako ndidzawapulumutsa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:25 Yesaya 2, ptsa. 149-151
25 Koma Yehova akunena kuti: “Ngakhale anthu amene agwidwa ndi munthu wamphamvu adzalandidwa,+Ndipo amene anagwidwa ndi wolamulira wankhanza adzapulumutsidwa.+ Ndidzalimbana ndi aliyense amene akulimbana nawe,+Ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.