-
Yesaya 51:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 “Ndimvereni, inu anthu amene mukufunafuna chilungamo,
Inu amene mukufunafuna Yehova.
Yangʼanani kuthanthwe limene munasemedwako,
Ndi pamalo okumbapo miyala pamene munakumbidwa.
-